Agoloso Presents - Atondido Stories Agoloso Presents - Beautiful Stories Click to read
  • Comments

Agoloso Presents - Atondido Stories

Agoloso Presents - Beautiful Stories

Published on in “Literary”, language — English. 251 pages.
Buku la Animal Farm linalembedwa mu 1946 ndi mlembi wa ku Mangalande, dzina lake George Orwell. Iye analemba bukuli mochenjera kwmbiri pofotokoza mavuto omwe ankachitika anthu ali pansi pa ulamuliro wachitsamunda komanso amene anadza anthuwo atayamba kudzilamulira okha. Wolemba bukuli ankaganizira kwambiri zimene zinachitika ku Russia. Mavuto amene anabenthula m’bukuli, anachitikanso m’maiko ambiri omwe analandira ufulu wodzilamulira. More

Other publications of “Agoloso Presents - Atondido Stories”

View all publications