Publié sur dans “Littéraire”, langue – English. 276 pages.
Buku la Animal Farm linalembedwa mu 1946 ndi mlembi wa
ku Mangalande, dzina lake George Orwell. Iye analemba bukuli
mochenjera kwmbiri pofotokoza mavuto omwe ankachitika
anthu ali pansi pa ulamuliro wachitsamunda komanso amene
anadza anthuwo atayamba kudzilamulira okha. Wolemba
bukuli ankaganizira kwambiri zimene zinachitika ku Russia.
Mavuto amene anabenthula m’bukuli, anachitikanso m’maiko
ambiri omwe analandira ufulu wodzilamulira. Plus