Agoloso Presents - Atondido Stories Agoloso Presents - Songs of Anisha Кликнуть для чтения
  • Комментарии

Agoloso Presents - Atondido Stories

Agoloso Presents - Songs of Anisha

Опубликовано в "Литература", язык - English. 193 страниц.
Buku la Animal Farm linalembedwa mu 1946 ndi mlembi wa ku Mangalande, dzina lake George Orwell. Iye analemba bukuli mochenjera kwmbiri pofotokoza mavuto omwe ankachitika anthu ali pansi pa ulamuliro wachitsamunda komanso amene anadza anthuwo atayamba kudzilamulira okha. Wolemba bukuli ankaganizira kwambiri zimene zinachitika ku Russia. Mavuto amene anabenthula m’bukuli, anachitikanso m’maiko ambiri omwe analandira ufulu wodzilamulira. Еще

Другие публикации «Agoloso Presents - Atondido Stories»

Посмотреть все публикации