Agoloso Presents - Atondido Stories Agoloso Presents - Ngale 2 Zum Anzeigen klicken
  • Kommentare

Agoloso Presents - Atondido Stories

Agoloso Presents - Ngale 2

Veröffentlicht am in "Literatur", Sprache — English. 70 Seiten.
Buku la Animal Farm linalembedwa mu 1946 ndi mlembi wa ku Mangalande, dzina lake George Orwell. Iye analemba bukuli mochenjera kwmbiri pofotokoza mavuto omwe ankachitika anthu ali pansi pa ulamuliro wachitsamunda komanso amene anadza anthuwo atayamba kudzilamulira okha. Wolemba bukuli ankaganizira kwambiri zimene zinachitika ku Russia. Mavuto amene anabenthula m’bukuli, anachitikanso m’maiko ambiri omwe analandira ufulu wodzilamulira. Mehr anzeigen

Andere Publikationen von "Agoloso Presents - Atondido Stories"

Alle Publikationen anzeigen