Agoloso Presents - Atondido Stories Agoloso Presents - Rodgers Dictionary of Proverbs Haga clic para leer
  • Comentarios

Agoloso Presents - Atondido Stories

Agoloso Presents - Rodgers Dictionary of Proverbs

Publicado el en “Literatura”, Idioma — English. 775 páginas.
Buku la Animal Farm linalembedwa mu 1946 ndi mlembi wa ku Mangalande, dzina lake George Orwell. Iye analemba bukuli mochenjera kwmbiri pofotokoza mavuto omwe ankachitika anthu ali pansi pa ulamuliro wachitsamunda komanso amene anadza anthuwo atayamba kudzilamulira okha. Wolemba bukuli ankaganizira kwambiri zimene zinachitika ku Russia. Mavuto amene anabenthula m’bukuli, anachitikanso m’maiko ambiri omwe analandira ufulu wodzilamulira. Más

Otras publicaciones de “Agoloso Presents - Atondido Stories”

Ver todas las publicaciones