Agoloso Presents - Atondido Stories Agoloso Presents - Rodgers Dictionary of Proverbs Cliquez pour lire
  • Commentaires

Agoloso Presents - Atondido Stories

Agoloso Presents - Rodgers Dictionary of Proverbs

Publié sur dans “Littéraire”, langue – English. 775 pages.
Buku la Animal Farm linalembedwa mu 1946 ndi mlembi wa ku Mangalande, dzina lake George Orwell. Iye analemba bukuli mochenjera kwmbiri pofotokoza mavuto omwe ankachitika anthu ali pansi pa ulamuliro wachitsamunda komanso amene anadza anthuwo atayamba kudzilamulira okha. Wolemba bukuli ankaganizira kwambiri zimene zinachitika ku Russia. Mavuto amene anabenthula m’bukuli, anachitikanso m’maiko ambiri omwe analandira ufulu wodzilamulira. Plus

Autres publications de “Agoloso Presents - Atondido Stories”

Voir toutes les publications